Levitiko 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Muzisunga masabata anga+ ndipo muzilemekeza* malo anga opatulika. Ine ndine Yehova. Numeri 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa mumsasa kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+ Numeri 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, aziphedwa kuti asakhalenso mumpingowo,+ chifukwa wadetsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera, choncho ndi wodetsedwa.
3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa mumsasa kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+
20 Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, aziphedwa kuti asakhalenso mumpingowo,+ chifukwa wadetsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera, choncho ndi wodetsedwa.