Levitiko 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwamuna akatulutsa umuna, azisamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+