Ekisodo 28:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Uwapangirenso makabudula ansalu ofika* mʼntchafu kuti azibisa maliseche awo.+