-
Ekisodo 39:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Anapanganso lamba wapamimba ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-