-
Ekisodo 30:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Akamalowa mʼchihema chokumanako, kapena akamapita kukatumikira paguwa lansembe, kukapereka kwa Yehova nsembe yowotcha pamoto, azisamba kuti asafe.
-