Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa. Yoswa 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova.
17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa.
14 Choncho muziopa Yehova ndi kumʼtumikira ndi mtima wathunthu* komanso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje* ndi ku Iguputo,+ ndipo muzitumikira Yehova.