Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.

  • Deuteronomo 12:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mʼmalomwake, mudzafunefune Yehova Mulungu wanu pamalo alionse amene adzasankhe kuti aikepo dzina lake komanso malo amene azidzakhala pakati pa mafuko anu onse, ndipo muzidzapita kumeneko.+ 6 Nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera mʼmanja mwanu,+ nsembe zimene mukupereka pokwaniritsa lonjezo, nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ngʼombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzapita nazo kumalo amenewo.+

  • Deuteronomo 12:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Samalani kuti musamadzapereke nsembe zanu zopsereza pamalo ena alionse amene mungaone.+ 14 Muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mʼdera limodzi mwa madera a mafuko anu, ndipo pamalo amenewo muzidzachita chilichonse chimene ndakulamulani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena