Levitiko 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Aliyense amene angadye nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Aliyense amene anganyamule nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
40 Aliyense amene angadye nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Aliyense amene anganyamule nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.