-
Levitiko 7:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma ngati nyama ya nsembeyo yatsala mpaka tsiku lachitatu, ayenera kuiwotcha pamoto.+ 18 Koma ngati nyama iliyonse ya nsembe yamgwirizano yadyedwa pa tsiku lachitatu, wopereka nsembeyo Mulungu sadzasangalala naye. Nsembe yakeyo idzakhala yopanda phindu. Idzakhala chinthu chonyansa, ndipo amene wadya nsembeyo adzayankha mlandu chifukwa cha kulakwa kwake.+
-