Miyambo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene amabera mwachinyengo munthu wosauka kuti awonjezere chuma chake+Komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera,Ndithu adzasauka. Maliko 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza,+ musabere munthu mwachinyengo+ ndiponso lakuti muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+
16 Amene amabera mwachinyengo munthu wosauka kuti awonjezere chuma chake+Komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera,Ndithu adzasauka.
19 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza,+ musabere munthu mwachinyengo+ ndiponso lakuti muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+