-
Levitiko 6:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndipo azibweretsa kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema kuti ikhale nsembe yake yakupalamula, yoperekedwa kwa Yehova, mogwirizana ndi mtengo umene wagamulidwa kuti ikhale nsembe yakupalamula.+ 7 Wansembe aziphimba machimo a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo adzakhululukidwa chilichonse chimene wachita chimene chapangitsa kuti apalamule mlandu.”+
-