Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amanyasidwa ndi masikelo achinyengo,Koma sikelo imene imayeza molondola imamusangalatsa.*+