Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mukalonjeza kanthu kwa Yehova Mulungu wanu+ musamachedwe kukwaniritsa zimene mwalonjezazo.+ Chifukwa Yehova Mulungu wanu adzafuna ndithu kuti mukwaniritse zimene mwalonjezazo. Mukapanda kutero mudzakhala kuti mwachimwa.+

  • Oweruza 11:30, 31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno Yefita analonjeza+ Yehova kuti: “Mukapereka Aamoni mʼmanja mwanga, 31 aliyense amene adzatuluka mʼnyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere kuchokera kwa Aamoni, ndidzamʼpereka kwa inu Yehova+ kuti akhale nsembe yopsereza.”+

  • 1 Samueli 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye analonjeza kuti: “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mukaona kuvutika kwa ine kapolo wanu nʼkundikumbukira ndiponso mukapanda kundiiwala ine kapolo wanu nʼkundipatsa mwana wamwamuna,+ ndidzamʼpereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake ndipo lezala silidzadutsa mʼmutu mwake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena