Genesis 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Rakele anati: “Mulungu wakhala woweruza wanga komanso wamva mawu anga, ndipo wandipatsa mwana wamwamuna.” Nʼchifukwa chake Rakele anapatsa mwanayo dzina lakuti Dani.*+
6 Ndiyeno Rakele anati: “Mulungu wakhala woweruza wanga komanso wamva mawu anga, ndipo wandipatsa mwana wamwamuna.” Nʼchifukwa chake Rakele anapatsa mwanayo dzina lakuti Dani.*+