Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 30:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi mchemwali wanga ndipo ndapambananso.” Choncho anapatsa mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+

  • Genesis 35:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ana amene Biliha kapolo wa Rakele anaberekera Yakobo anali Dani ndi Nafitali.

  • Genesis 46:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ana a Nafitali+ anali Yahazeeli, Guni, Yezera ndi Silemu.+

  • 1 Mbiri 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana a Nafitali+ anali Yazieli, Guni, Yezera ndi Salumu ndipo anali mbadwa za Biliha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena