Ekisodo 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita mʼtsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.* Anthu onse amene anawerengedwa analipo 603,550.+ Numeri 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anthu onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+ Numeri 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Anthu a fuko la Levi okha usawalembe mayina, ndipo usaphatikize chiwerengero chawo pamodzi ndi cha Aisiraeli enawo.+ Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona mʼchipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita mʼtsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli potengera muyezo wa sekeli lakumalo oyera.* Anthu onse amene anawerengedwa analipo 603,550.+
49 “Anthu a fuko la Levi okha usawalembe mayina, ndipo usaphatikize chiwerengero chawo pamodzi ndi cha Aisiraeli enawo.+
29 Mitembo yanu idzagona mʼchipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+