Ekisodo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzaike Urimu ndi Tumimu*+ mʼchovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamakaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula pamtima pake zinthu zogwiritsa ntchito poweruza Aisiraeli akamaonekera kwa Yehova nthawi zonse. 1 Samueli 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Davide atadziwa kuti Sauli akumukonzera chiwembu, anauza Abiyatara wansembe kuti: “Bweretsa efodi.”+ 1 Samueli 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli ankafunsira kwa Yehova+ koma Yehova sankamuyankha, kaya kudzera mʼmaloto, Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri. Nehemiya 7:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Bwanamkubwa*+ anawauza kuti asamadye zinthu zopatulika koposa,+ mpaka patakhala wansembe amene angagwiritse ntchito Urimu ndi Tumimu.+
30 Udzaike Urimu ndi Tumimu*+ mʼchovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamakaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula pamtima pake zinthu zogwiritsa ntchito poweruza Aisiraeli akamaonekera kwa Yehova nthawi zonse.
9 Davide atadziwa kuti Sauli akumukonzera chiwembu, anauza Abiyatara wansembe kuti: “Bweretsa efodi.”+
6 Sauli ankafunsira kwa Yehova+ koma Yehova sankamuyankha, kaya kudzera mʼmaloto, Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.
65 Bwanamkubwa*+ anawauza kuti asamadye zinthu zopatulika koposa,+ mpaka patakhala wansembe amene angagwiritse ntchito Urimu ndi Tumimu.+