Numeri 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,* ndipo uike dzanja lako pa iye.+
18 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,* ndipo uike dzanja lako pa iye.+