Levitiko 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati akupereka nkhosa kapena mbuzi+ kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka mwana wamphongo wopanda chilema.+ Levitiko 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno azitsuka matumbo komanso ziboda ndi madzi. Kenako wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.
10 Ngati akupereka nkhosa kapena mbuzi+ kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka mwana wamphongo wopanda chilema.+
13 Ndiyeno azitsuka matumbo komanso ziboda ndi madzi. Kenako wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.