Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzidya mkate wopanda zofufumitsa kwa masiku 7.+ Pa tsiku loyamba muzichotsa mʼnyumba zanu ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa chifukwa aliyense wodya mkate wokhala ndi zofufumitsa, kuchokera pa tsiku loyamba kukafika pa tsiku la 7, munthu wochita zimenezi aziphedwa kuti asakhalenso mu Isiraeli.

  • Levitiko 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pa tsiku la 15 la mwezi umenewu, muzichitira Yehova Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda zofufumitsa kwa masiku 7.+

  • 1 Akorinto 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho tiyeni tichite Chikondwerero cha Pasikachi,+ osati ndi zofufumitsa zakale, kapena zofufumitsa zoimira zoipa ndi uchimo, koma ndi mkate wopanda zofufumitsa woimira kuona mtima ndi choonadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena