Ekisodo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Muzichita Chikondwerero cha Masabata,* ndipo pochita chikondwerero chimenechi muzipereka tirigu woyamba kucha pa tirigu amene mwakolola. Kumapeto kwa chaka muzichita Chikondwerero cha Zokolola.*+ Deuteronomo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno muzichitira Yehova Mulungu wanu Chikondwerero cha Masabata,+ popereka nsembe zaufulu zimene mungathe, mogwirizana ndi mmene Yehova Mulungu wanu wakudalitsirani.+ Machitidwe 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano onse anali atasonkhana pamodzi pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite.+
22 Muzichita Chikondwerero cha Masabata,* ndipo pochita chikondwerero chimenechi muzipereka tirigu woyamba kucha pa tirigu amene mwakolola. Kumapeto kwa chaka muzichita Chikondwerero cha Zokolola.*+
10 Ndiyeno muzichitira Yehova Mulungu wanu Chikondwerero cha Masabata,+ popereka nsembe zaufulu zimene mungathe, mogwirizana ndi mmene Yehova Mulungu wanu wakudalitsirani.+