Levitiko 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+ Levitiko 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa tsiku limeneli muzilengeza+ kuti kuli msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale mʼmibadwo yanu yonse.
16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+
21 Pa tsiku limeneli muzilengeza+ kuti kuli msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale mʼmibadwo yanu yonse.