-
Levitiko 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Popereka mitanda ya mkateyi muziperekanso ana a nkhosa amphongo opanda chilema okwana 7, aliyense wa chaka chimodzi, komanso ngʼombe imodzi yaingʼono yamphongo ndi nkhosa ziwiri zamphongo.+ Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe yopsereza, nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova. Ziziperekedwa pamodzi ndi nsembe yambewu ndi nsembe zachakumwa kuti zikhale kafungo kosangalatsa* kwa Yehova.
-