Ezara 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anachita Chikondwerero cha Misasa mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.+ Tsiku ndi tsiku ankapereka nsembe zopsereza zomwe zinkayenera kuperekedwa tsiku lililonse.+
4 Kenako anachita Chikondwerero cha Misasa mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.+ Tsiku ndi tsiku ankapereka nsembe zopsereza zomwe zinkayenera kuperekedwa tsiku lililonse.+