Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu! Yesaya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi wokonzeka kusonyeza mkwiyo wake.+ Yehova amabwezera adani ake,Ndipo adani ake amawasungira mkwiyo.
94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!
24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi wokonzeka kusonyeza mkwiyo wake.+ Yehova amabwezera adani ake,Ndipo adani ake amawasungira mkwiyo.