Numeri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anafa ndi mliriwo analipo 24,000.+ 1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso tisamachite chiwerewere,* mmene ena a iwo anachitira, nʼkufa anthu 23,000 tsiku limodzi.+