Deuteronomo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Samalani kuti musakanyalanyaze Mlevi+ kwa nthawi yonse imene mukakhale mʼdzikolo.