Ekisodo 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga* khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+
36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga* khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+