Yoswa 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Yoswa analanda dziko lonse mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza Mose.+ Kenako Yoswa anagawa dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo, mogwirizana ndi mafuko awo.+ Ndipo mʼdziko lonselo munalibenso nkhondo.+ Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+ Salimo 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo dziko lawo munalipereka kwa makolo athu.+ Munagonjetsa mitundu ya anthu nʼkuithamangitsa.+
23 Choncho Yoswa analanda dziko lonse mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza Mose.+ Kenako Yoswa anagawa dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo, mogwirizana ndi mafuko awo.+ Ndipo mʼdziko lonselo munalibenso nkhondo.+
18 Kenako gulu lonse la Aisiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamanga chihema chokumanako,+ popeza pa nthawiyo nʼkuti atagonjetsa dzikolo.+
2 Munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo dziko lawo munalipereka kwa makolo athu.+ Munagonjetsa mitundu ya anthu nʼkuithamangitsa.+