Yoswa 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Panopa Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+ Choncho bwererani, mupite kumatenti anu kudera limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani, kutsidya lina* la Yorodano.+ Yoswa 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali Aisiraeli mʼdziko la Kanani. Anabwerera ku Giliyadi,+ kudera limene Mose anawapatsa molamulidwa ndi Yehova kuti azikhalako.+
4 Panopa Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+ Choncho bwererani, mupite kumatenti anu kudera limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani, kutsidya lina* la Yorodano.+
9 Zitatero, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali Aisiraeli mʼdziko la Kanani. Anabwerera ku Giliyadi,+ kudera limene Mose anawapatsa molamulidwa ndi Yehova kuti azikhalako.+