Yoswa 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi komanso hafu ya fuko la Manase, anawoloka nʼkumayenda patsogolo pa Aisiraeli ena atakonzekera kumenya nkhondo,+ ngati mmene Mose anawalangizira.+
12 Anthu a fuko la Rubeni, a fuko la Gadi komanso hafu ya fuko la Manase, anawoloka nʼkumayenda patsogolo pa Aisiraeli ena atakonzekera kumenya nkhondo,+ ngati mmene Mose anawalangizira.+