Yoswa 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mose anali atapatsa hafu ya fuko la Manase cholowa chawo ku Basana.+ Hafu ina ya fukolo, Yoswa anaipatsa cholowa pamodzi ndi abale awo kutsidya lina la Yorodano kumadzulo.+ Komanso pamene Yoswa ankawauza kuti azipita kumatenti awo, anawadalitsa.
7 Mose anali atapatsa hafu ya fuko la Manase cholowa chawo ku Basana.+ Hafu ina ya fukolo, Yoswa anaipatsa cholowa pamodzi ndi abale awo kutsidya lina la Yorodano kumadzulo.+ Komanso pamene Yoswa ankawauza kuti azipita kumatenti awo, anawadalitsa.