Deuteronomo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako tinalanda mizinda yake yonse. Panalibe mzinda umene sitinaulande. Tinalanda mizinda 60 mʼchigawo chonse cha Arigobi, mʼdera lonse la ufumu wa Ogi ku Basana.+
4 Kenako tinalanda mizinda yake yonse. Panalibe mzinda umene sitinaulande. Tinalanda mizinda 60 mʼchigawo chonse cha Arigobi, mʼdera lonse la ufumu wa Ogi ku Basana.+