Ekisodo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Mulungu anachititsa kuti Aisiraeli adutse njira yaitali yodzera mʼchipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma potuluka mʼdziko la Iguputo, Aisiraeli anayenda mwadongosolo ngati magulu a asilikali.
18 Choncho Mulungu anachititsa kuti Aisiraeli adutse njira yaitali yodzera mʼchipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma potuluka mʼdziko la Iguputo, Aisiraeli anayenda mwadongosolo ngati magulu a asilikali.