Yoswa 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi ndinatumiza Mose ndi Aroni+ ndipo ndinachititsa kuti ku Iguputo kugwe miliri.+ Kenako ndinakutulutsani ku Iguputoko. 1 Samueli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+
5 Patapita nthawi ndinatumiza Mose ndi Aroni+ ndipo ndinachititsa kuti ku Iguputo kugwe miliri.+ Kenako ndinakutulutsani ku Iguputoko.
8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+