Genesis 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yosefe anauza bambo ake ndi abale akewo kuti azikhala ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino kwambiri adzikolo ku Ramese*+ monga mmene Farao analamulira. Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
11 Choncho Yosefe anauza bambo ake ndi abale akewo kuti azikhala ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino kwambiri adzikolo ku Ramese*+ monga mmene Farao analamulira.
37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+