Ekisodo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwezi uno uzikhala mwezi wanu woyamba pa chaka. Chaka chanu chiziyamba ndi mwezi uno.+ Ekisodo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukutuluka mu Iguputo lero, mʼmwezi wa Abibu.*+