Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
37 Kenako Aisiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Panali amuna oyenda pansi pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+