Numeri 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Kwera phiri ili la Abarimu,+ ukaone dziko limene ndidzalipereke kwa Aisiraeli.+ Deuteronomo 32:48, 49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova analankhula ndi Mose pa tsiku lomweli kuti: 49 “Kwera mʼphiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili mʼdziko la Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa Aisiraeli kuti likhale lawo.+
12 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Kwera phiri ili la Abarimu,+ ukaone dziko limene ndidzalipereke kwa Aisiraeli.+
48 Yehova analankhula ndi Mose pa tsiku lomweli kuti: 49 “Kwera mʼphiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili mʼdziko la Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa Aisiraeli kuti likhale lawo.+