Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+ Salimo 106:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwowa sanawononge mitundu ina ya anthu,+Ngati mmene Yehova anawalamulira.+
21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+