Numeri 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo. Numeri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nʼzimenenso makolo anu anachita ku Kadesi-barinea, nditawatuma kuti akafufuze dziko.+
26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo.