Numeri 33:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, nʼkukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu. Deuteronomo 32:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Kenako ukafera paphiri limene ukufuna kukwerali nʼkuikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako,* mofanana ndi Aroni mʼbale wako amene anafera paphiri la Hora+ nʼkuikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.
37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, nʼkukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.
50 Kenako ukafera paphiri limene ukufuna kukwerali nʼkuikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako,* mofanana ndi Aroni mʼbale wako amene anafera paphiri la Hora+ nʼkuikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.