Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi amene anasankhidwa pa gulu la anthuwo. Iwo anali atsogoleri+ a mafuko a makolo awo, atsogoleri a anthu masauzande mu Isiraeli.”+
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
16 Amenewa ndi amene anasankhidwa pa gulu la anthuwo. Iwo anali atsogoleri+ a mafuko a makolo awo, atsogoleri a anthu masauzande mu Isiraeli.”+