Genesis 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkwiyo wawo ukhale wotembereredwa chifukwa ndi wankhanza, komanso ukali wawo chifukwa umachita zinthu mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+
7 Mkwiyo wawo ukhale wotembereredwa chifukwa ndi wankhanza, komanso ukali wawo chifukwa umachita zinthu mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+