Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+ Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “Nʼchiyani chimene wachitachi? Tamvetsera, magazi a mʼbale wako akundilirira munthaka.+ Salimo 106:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa. Luka 11:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Choncho mʼbadwo uwu udzaimbidwa mlandu wa magazi a aneneri, amene anakhetsedwa kuyambira pamene dziko linakhazikika.+
8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+
10 Pamenepo Mulungu anati: “Nʼchiyani chimene wachitachi? Tamvetsera, magazi a mʼbale wako akundilirira munthaka.+
38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.
50 Choncho mʼbadwo uwu udzaimbidwa mlandu wa magazi a aneneri, amene anakhetsedwa kuyambira pamene dziko linakhazikika.+