Numeri 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana a Merari, potengera mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Mabanja a Alevi anali amenewa potengera nyumba za makolo awo. Numeri 26:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Mabanja a Alevi ndi awa: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi+ ndi banja la Akora.+ Kohati anabereka Amuramu.+
20 Ana a Merari, potengera mabanja awo, anali Mali+ ndi Musi.+ Mabanja a Alevi anali amenewa potengera nyumba za makolo awo.
58 Mabanja a Alevi ndi awa: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi+ ndi banja la Akora.+ Kohati anabereka Amuramu.+