-
Ekisodo 26:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Katani imeneyi uipachike pazipilala 4 za mtengo wa mthethe zokutidwa ndi golide. Tizitsulo tokolowekapo kataniyi tikhale tagolide. Zipilala zimenezi zikhale pazitsulo 4 zasiliva.
-
-
Ekisodo 36:37, 38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Atatero anawomba nsalu yotchinga khomo la chihema. Nsaluyo inali ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ 38 Anapanganso zipilala zake 5 ndi tizitsulo take tokolowekapo nsalu yotchingayo. Pamwamba pa zipilalazo anakutapo ndi golide komanso tizitsulo take tolumikizira anatikuta ndi golide. Koma zitsulo zake 5 zokhazikapo zipilalazo zinali zakopa.
-