-
Ekisodo 27:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Upangenso zipilala zake 20 ndi zitsulo 20 zakopa zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo ta zipilala tokolowekapo nsalu ndi tolumikizira take tikhale tasiliva. 11 Nsalu yambali yakumpoto kwa mpandawo ikhalenso mamita 45 mulitali mwake, ndipo kukhale zipilala 20 ndi zitsulo 20 zakopa zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo tokolowekapo nsalu ndi tolumikizira take tikhale tasiliva.
-