1 Mbiri 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita mʼtsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense mmodzi ndi mmodzi* ndipo onse anakwana 38,000. Luka 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwanawa Yosefe,+mwana wa Heli,
3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita mʼtsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense mmodzi ndi mmodzi* ndipo onse anakwana 38,000.
23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwanawa Yosefe,+mwana wa Heli,