-
Ekisodo 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Nsalu yambali yakumpoto kwa mpandawo ikhalenso mamita 45 mulitali mwake, ndipo kukhale zipilala 20 ndi zitsulo 20 zakopa zokhazikapo zipilalazo. Tizitsulo tokolowekapo nsalu ndi tolumikizira take tikhale tasiliva.
-